Ekisodo 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Magaleta a Farao ndi gulu lake lankhondo wawaponyera mʼnyanja.+Asilikali odalirika a Farao amira mʼNyanja Yofiira.+
4 Magaleta a Farao ndi gulu lake lankhondo wawaponyera mʼnyanja.+Asilikali odalirika a Farao amira mʼNyanja Yofiira.+