Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Choncho mudziwe lero, ndipo muzikumbukira mumtima mwanu kuti Yehova ndi Mulungu woona, kumwamba ndiponso padziko lapansi.+ Palibenso wina.+

  • Yesaya 44:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Musachite mantha,

      Ndipo musathedwe nzeru chifukwa cha mantha.+

      Kodi sindinauziretu aliyense wa inu ndi kulengeza zimenezi?

      Inu ndinu mboni zanga.+

      Kodi palinso Mulungu wina kupatulapo ine?

      Ayi, palibe Thanthwe lina.+ Palibe lina limene ndikulidziwa.’”

  • Maliko 12:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mlembiyo ananena kuti: “Mphunzitsi, mwanena bwino mogwirizana ndi choonadi, ‘Iye ndi Mmodzi ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo iyeyo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena