Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Choncho mudziwe lero, ndipo muzikumbukira mumtima mwanu kuti Yehova ndi Mulungu woona, kumwamba ndiponso padziko lapansi.+ Palibenso wina.+

  • Deuteronomo 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tamverani, Aisiraeli inu: Yehova Mulungu wathu ndi Yehova mmodzi.+

  • Yesaya 45:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Lankhulani ndipo mufotokoze mlandu wanu.

      Mukambirane mogwirizana.

      Kodi ndi ndani ananeneratu zimenezi kalekale

      Nʼkuzilengeza kuyambira kalekale?

      Kodi si ine, Yehova?

      Palibenso Mulungu wina koma ine ndekha.

      Ine ndi Mulungu wolungama komanso Mpulumutsi+ ndipo palibenso wina kupatulapo ine.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena