Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+ Yesaya 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chilungamo changa chayandikira.+ Chipulumutso changa chikubwera kwa iwe+Ndipo manja anga adzaweruza mitundu ya anthu.+ Zilumba zidzayembekezera ine+Ndipo zidzadikira dzanja langa.* Yesaya 62:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Taonani! Yehova walengeza mpaka kumalekezero a dziko lapansi kuti: “Mwana wamkazi wa Ziyoni* mumuuze kuti,‘Taona! Chipulumutso chako chikubwera.+ Taona! Mphoto yake ili ndi iyeyo,Ndipo malipiro amene amapereka ali pamaso pake.’”+
2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
5 Chilungamo changa chayandikira.+ Chipulumutso changa chikubwera kwa iwe+Ndipo manja anga adzaweruza mitundu ya anthu.+ Zilumba zidzayembekezera ine+Ndipo zidzadikira dzanja langa.*
11 Taonani! Yehova walengeza mpaka kumalekezero a dziko lapansi kuti: “Mwana wamkazi wa Ziyoni* mumuuze kuti,‘Taona! Chipulumutso chako chikubwera.+ Taona! Mphoto yake ili ndi iyeyo,Ndipo malipiro amene amapereka ali pamaso pake.’”+