Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 44:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Fuulani mosangalala kumwamba inu,

      Chifukwa Yehova wachita zimenezi.

      Fuulani posonyeza kupambana, inu malo otsika kwambiri a dziko lapansi.

      Mapiri inu, fuulani mosangalala,+

      Iwe nkhalango ndi inu mitengo yonse imene ili mmenemo,

      Chifukwa Yehova wawombola Yakobo,

      Ndipo wasonyeza kukongola kwake pa Isiraeli.”+

  • Yesaya 60:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.

      Adzatenga dzikoli kukhala lawo mpaka kalekale.

      Anthuwo ndi mmera umene ndinadzala,

      Ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndioneke kukongola.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena