Yesaya 41:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Usachite mantha, nyongolotsi* iwe Yakobo,+Inu amuna a mu Isiraeli, ineyo ndikuthandizani,” akutero Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli. Yesaya 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wako,Woyera wa Isiraeli, Mpulumutsi wako. Ndapereka Iguputo kuti akhale dipo* lako.Ndaperekanso Itiyopiya ndi Seba mʼmalo mwa iwe. Yesaya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+
14 “Usachite mantha, nyongolotsi* iwe Yakobo,+Inu amuna a mu Isiraeli, ineyo ndikuthandizani,” akutero Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli.
3 Chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wako,Woyera wa Isiraeli, Mpulumutsi wako. Ndapereka Iguputo kuti akhale dipo* lako.Ndaperekanso Itiyopiya ndi Seba mʼmalo mwa iwe.
6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+