Yesaya 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Babulo, amene ndi waulemerero kwambiri* kuposa maufumu onse,+Chinthu chokongola chimene Akasidi amachinyadira,+Adzakhala ngati Sodomu ndi Gomora pa nthawi imene Mulungu anawononga mizindayi.+ Yesaya 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 mudzanena mwambi uwu wonyoza mfumu ya Babulo: “Amene ankagwiritsa ntchito anzake mokakamiza uja wawonongedwa! Kuponderezedwa kuja kwatha ndithu!+ Chivumbulutso 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pachipumi pake panalembedwa dzina lachinsinsi lakuti: “Babulo Wamkulu, mayi wa mahule+ ndiponso mayi wa zonyansa zapadziko lapansi.”+
19 Babulo, amene ndi waulemerero kwambiri* kuposa maufumu onse,+Chinthu chokongola chimene Akasidi amachinyadira,+Adzakhala ngati Sodomu ndi Gomora pa nthawi imene Mulungu anawononga mizindayi.+
4 mudzanena mwambi uwu wonyoza mfumu ya Babulo: “Amene ankagwiritsa ntchito anzake mokakamiza uja wawonongedwa! Kuponderezedwa kuja kwatha ndithu!+
5 Pachipumi pake panalembedwa dzina lachinsinsi lakuti: “Babulo Wamkulu, mayi wa mahule+ ndiponso mayi wa zonyansa zapadziko lapansi.”+