Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 5:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse. Akanachita zimenezi zinthu zikanawayendera bwino, iwowo ndi ana awo mpaka kalekale!+

  • Salimo 81:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Zikanakhala bwino ngati anthu anga akanandimvera,+

      Zikanakhala bwino ngati Isiraeli akanayenda mʼnjira zanga.+

      14 Ndikanagonjetsa adani awo mofulumira,

      Ndikanalanga adani awo ndi dzanja langa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena