Yoswa 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano ine ndatsala pangʼono kufa. Inu mukudziwa bwino ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse, kuti palibe mawu ngakhale amodzi pa malonjezo onse abwino amene Yehova Mulungu wanu ananena, omwe sanakwaniritsidwe. Onse akwaniritsidwa kwa inu. Palibe ngakhale mawu amodzi omwe sanakwaniritsidwe.+ Yesaya 45:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndalumbira pa dzina langa.Mawu amene atuluka pakamwa panga ndi olondola,Ndipo adzakwaniritsidwa ndithu:+ Bondo lililonse lidzandigwadira,Ndipo lilime lililonse lidzalumbira kuti lidzakhala lokhulupirika kwa ine,+
14 Tsopano ine ndatsala pangʼono kufa. Inu mukudziwa bwino ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse, kuti palibe mawu ngakhale amodzi pa malonjezo onse abwino amene Yehova Mulungu wanu ananena, omwe sanakwaniritsidwe. Onse akwaniritsidwa kwa inu. Palibe ngakhale mawu amodzi omwe sanakwaniritsidwe.+
23 Ndalumbira pa dzina langa.Mawu amene atuluka pakamwa panga ndi olondola,Ndipo adzakwaniritsidwa ndithu:+ Bondo lililonse lidzandigwadira,Ndipo lilime lililonse lidzalumbira kuti lidzakhala lokhulupirika kwa ine,+