Yesaya 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu amene Yehova anawawombola adzabwerera+ ndipo adzafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Chisangalalo chosatha chidzakhala ngati chisoti chachifumu kumutu kwawo.+ Adzakhala okondwa ndi osangalalaNdipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+
10 Anthu amene Yehova anawawombola adzabwerera+ ndipo adzafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Chisangalalo chosatha chidzakhala ngati chisoti chachifumu kumutu kwawo.+ Adzakhala okondwa ndi osangalalaNdipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+