Yesaya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+Anthu olemedwa ndi zolakwa,Ana a anthu ochita zoipa, ana a makhalidwe oipa. Iwo asiya Yehova.+Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu.Iwo atembenuka nʼkumusiya. Yesaya 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa iwo ndi anthu opanduka,+ ana ochita zachinyengo,+Ana amene safuna kumva malamulo* a Yehova,+
4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+Anthu olemedwa ndi zolakwa,Ana a anthu ochita zoipa, ana a makhalidwe oipa. Iwo asiya Yehova.+Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu.Iwo atembenuka nʼkumusiya.
9 Chifukwa iwo ndi anthu opanduka,+ ana ochita zachinyengo,+Ana amene safuna kumva malamulo* a Yehova,+