Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 14:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Muzidzadya chakhumi cha mbewu zanu, kumwa vinyo wanu watsopano, kudya mafuta anu, ana oyamba a ngʼombe ndi a nkhosa zanu pamaso pa Yehova Mulungu wanu, pamalo amene iye adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Muzidzachita zimenezi kuti mudzaphunzire kuopa Yehova Mulungu wanu nthawi zonse.+

  • Yesaya 65:21, 22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iwo adzamanga nyumba nʼkumakhalamo,+

      Ndipo adzadzala minda ya mpesa nʼkudya zipatso zake.+

      22 Sadzamanga nyumba kuti wina azikhalamo,

      Kapena kudzala kuti ena adye.

      Chifukwa masiku a anthu anga adzakhala ngati masiku a mtengo,+

      Ndipo anthu anga osankhidwa adzasangalala mokwanira ndi ntchito ya manja awo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena