Ekisodo 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno mngelo wa Mulungu woona+ amene ankayenda patsogolo pa Aisiraeli anachoka nʼkupita kumbuyo kwawo. Ndipo chipilala cha mtambo chija chinachoka kutsogolo nʼkukaima kumbuyo kwawo.+ Ekisodo 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndikukutumizirani mngelo patsogolo panu+ kuti azikutetezani mʼnjira komanso kukakulowetsani mʼdziko limene ndakukonzerani.+
19 Ndiyeno mngelo wa Mulungu woona+ amene ankayenda patsogolo pa Aisiraeli anachoka nʼkupita kumbuyo kwawo. Ndipo chipilala cha mtambo chija chinachoka kutsogolo nʼkukaima kumbuyo kwawo.+
20 Ndikukutumizirani mngelo patsogolo panu+ kuti azikutetezani mʼnjira komanso kukakulowetsani mʼdziko limene ndakukonzerani.+