Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma ngati simudzandimvera kapena kutsatira malamulo onsewa,+

  • Levitiko 26:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ine ndidzakukanani, ndipo adani anu adzakugonjetsani+ ndi kukuponderezani,+ moti muzidzathawa popanda munthu wokuthamangitsani.+

  • Deuteronomo 28:63
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 63 Mofanana ndi mmene Yehova anasangalalira kuchititsa kuti zinthu zikuyendereni bwino komanso kuchititsa kuti muchuluke, Yehova adzasangalalanso kuti akuwonongeni nʼkukufafanizani, ndipo mudzatheratu mʼdziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena