Ekisodo 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Aisiraeli mʼmanja mwa Aiguputo,+ ndipo Aisiraeli anaona Aiguputo atafa mʼmphepete mwa nyanja. Yesaya 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unapangitsa kuti pansi pa nyanja pakhale njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+
30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Aisiraeli mʼmanja mwa Aiguputo,+ ndipo Aisiraeli anaona Aiguputo atafa mʼmphepete mwa nyanja.
10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unapangitsa kuti pansi pa nyanja pakhale njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+