Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Tsopano uona zimene ndichite kwa Farao.+ Dzanja langa lamphamvu limukakamiza kuti awalole kuchoka, ndipo dzanja langa lamphamvu limukakamiza kuti awathamangitse mʼdziko lake.”+

  • Ekisodo 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho uwauze Aisiraeli kuti, ‘Ine ndine Yehova. Ndidzakupulumutsani ku ntchito yokakamiza imene Aiguputo akukugwiritsani ndipo ndidzakulanditsani kuti musakhalenso akapolo awo.+ Ndidzakuwombolani ndi dzanja langa lotambasula* komanso ndi ziweruzo zamphamvu.+

  • Ekisodo 15:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+

      Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala ngati mwala, osachita kanthu.

      Mpaka anthu anu atadutsa, inu Yehova,

      Mpaka anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena