Ekisodo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala chete ngati mwala.Kufikira anthu anu+ atadutsa, inu Yehova,Kufikira anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+
16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala chete ngati mwala.Kufikira anthu anu+ atadutsa, inu Yehova,Kufikira anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+