Chivumbulutso 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno ndinaona kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano,+ chifukwa kumwamba kwakale ndi dziko lapansi lakale zinali zitachoka+ ndipo kulibenso nyanja.+ Chivumbulutso 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye adzapukuta misozi yonse mʼmaso mwawo+ ndipo imfa sidzakhalaponso.+ Sipadzakhalanso kulira, kubuula kapena kupweteka.+ Zakalezo zapita.”
21 Ndiyeno ndinaona kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano,+ chifukwa kumwamba kwakale ndi dziko lapansi lakale zinali zitachoka+ ndipo kulibenso nyanja.+
4 Iye adzapukuta misozi yonse mʼmaso mwawo+ ndipo imfa sidzakhalaponso.+ Sipadzakhalanso kulira, kubuula kapena kupweteka.+ Zakalezo zapita.”