Yesaya 65:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Taonani! Ndikulenga kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano.+Ndipo zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso,Kapena kuvutitsa maganizo.+ Yesaya 66:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Chifukwa kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzapitiriza kukhala pamaso panga. Mofanana ndi zimenezi, ana anu* ndi dzina lanu zidzapitiriza kukhalapo,”+ akutero Yehova. 2 Petulo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma pali kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano zimene ife tikuyembekezera mogwirizana ndi lonjezo lake,+ ndipo mmenemo mudzakhala chilungamo.+
17 Taonani! Ndikulenga kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano.+Ndipo zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso,Kapena kuvutitsa maganizo.+
22 “Chifukwa kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzapitiriza kukhala pamaso panga. Mofanana ndi zimenezi, ana anu* ndi dzina lanu zidzapitiriza kukhalapo,”+ akutero Yehova.
13 Koma pali kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano zimene ife tikuyembekezera mogwirizana ndi lonjezo lake,+ ndipo mmenemo mudzakhala chilungamo.+