Aroma 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso Yesaya anati: “Padzakhala muzu wa Jese,+ winawake amene adzatuluke kuti alamulire mitundu.+ Chiyembekezo cha anthu a mitundu ina chidzakhala pa iyeyo.”+ Chivumbulutso 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kuti adzachitire umboni zinthu zimenezi kwa iwe kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu komanso mbadwa ya Davide.+ Ndinenso nthanda yowala kwambiri.’”+
12 Komanso Yesaya anati: “Padzakhala muzu wa Jese,+ winawake amene adzatuluke kuti alamulire mitundu.+ Chiyembekezo cha anthu a mitundu ina chidzakhala pa iyeyo.”+
16 ‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kuti adzachitire umboni zinthu zimenezi kwa iwe kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu komanso mbadwa ya Davide.+ Ndinenso nthanda yowala kwambiri.’”+