Yesaya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthambi+ idzaphuka pachitsa cha Jese,+Ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzabereka zipatso. Yesaya 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa tsiku limenelo muzu wa Jese+ udzaimirira ngati chizindikiro kwa anthu.+ Anthu a mitundu ina adzatembenukira kwa iye kuti awapatse malangizo,*+Ndipo malo ake okhalapo adzakhala aulemerero. Mateyu 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndithudi, mʼdzina lake mitundu ya anthu idzayembekezera zabwino.”+
10 Pa tsiku limenelo muzu wa Jese+ udzaimirira ngati chizindikiro kwa anthu.+ Anthu a mitundu ina adzatembenukira kwa iye kuti awapatse malangizo,*+Ndipo malo ake okhalapo adzakhala aulemerero.