-
Yeremiya 22:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Yehova wanena kuti: “Muzichita zinthu motsatira malamulo komanso mwachilungamo. Muzipulumutsa munthu amene akuberedwa mʼmanja mwa munthu wakuba mwachinyengo. Musamachitire nkhanza mlendo aliyense amene akukhala mʼdziko lanu ndipo musamavulaze mwana wamasiye kapena mkazi wamasiye.+ Musamakhetse magazi a munthu aliyense wosalakwa mumzinda uno.+
-