Deuteronomo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti anthu a Yehova ndi gawo lake.+Yakobo ndiye cholowa chake.+ Salimo 115:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akutikumbukira ndipo adzatidalitsa.Adzadalitsa nyumba ya Isiraeli.+Adzadalitsa nyumba ya Aroni. Yesaya 61:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana awo* adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+Ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Anthu onse owaona adzawazindikira,Kuti ndi ana amene* Yehova anawadalitsa.”+
12 Yehova akutikumbukira ndipo adzatidalitsa.Adzadalitsa nyumba ya Isiraeli.+Adzadalitsa nyumba ya Aroni.
9 Ana awo* adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+Ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Anthu onse owaona adzawazindikira,Kuti ndi ana amene* Yehova anawadalitsa.”+