Yesaya 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Inu Yehova ndinu Mulungu wanga. Ndikukukwezani ndi kutamanda dzina lanuChifukwa mwachita zinthu zodabwitsa,+Zinthu zimene munali ndi cholinga choti muzichite kuyambira kalekale,+Mwazichita mokhulupirika+ komanso modalirika.
25 Inu Yehova ndinu Mulungu wanga. Ndikukukwezani ndi kutamanda dzina lanuChifukwa mwachita zinthu zodabwitsa,+Zinthu zimene munali ndi cholinga choti muzichite kuyambira kalekale,+Mwazichita mokhulupirika+ komanso modalirika.