Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 40:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Inu Yehova Mulungu wanga,

      Mwatichitira zinthu zambiri zodabwitsa+

      Ndipo mumatiganizira.+

      Palibe angafanane ndi inu.

      Nditati ndilankhule kapena kunena za zodabwitsazo,

      Zingakhale zochuluka kwambiri moti sindingathe kuzifotokoza.+

  • Salimo 98:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 98 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+

      Chifukwa wachita zinthu zodabwitsa.+

      Dzanja lake lamanja, mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.*+

  • Salimo 107:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Anthu ayamike Yehova+ chifukwa cha chikondi chake chokhulupirika,

      Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu.+

  • Salimo 145:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 145 Ndidzakukwezani, inu Mfumu ndi Mulungu wanga,+

      Ndidzatamanda dzina lanu kwamuyaya.+

  • Salimo 145:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Anthu adzatamanda ntchito zanu ku mibadwomibadwo.

      Adzanena za ntchito zanu zamphamvu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena