Salimo 132:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa Yehova wasankha Ziyoni.+Akufunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye akuti:+ 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka kalekale.Ndidzakhala mmenemu,+ chifukwa zimenezi ndi zimene ndikulakalaka. Yesaya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Fuulani mwachisangalalo inu okhala mu Ziyoni,*Chifukwa Woyera wa Isiraeli amene ali pakati panu ndi wamkulu.”
13 Chifukwa Yehova wasankha Ziyoni.+Akufunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye akuti:+ 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka kalekale.Ndidzakhala mmenemu,+ chifukwa zimenezi ndi zimene ndikulakalaka.
6 Fuulani mwachisangalalo inu okhala mu Ziyoni,*Chifukwa Woyera wa Isiraeli amene ali pakati panu ndi wamkulu.”