Yesaya 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawi imeneyo, munthu wolumala adzadumpha ngati mmene imachitira mbawala,+Ndipo lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mosangalala.+ Mʼchipululu mudzatumphuka madzi,Ndipo mʼdera lachipululu mudzayenda mitsinje.
6 Pa nthawi imeneyo, munthu wolumala adzadumpha ngati mmene imachitira mbawala,+Ndipo lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mosangalala.+ Mʼchipululu mudzatumphuka madzi,Ndipo mʼdera lachipululu mudzayenda mitsinje.