Yesaya 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawiyo, munthu wolumala adzakwera phiri ngati mmene imachitira mbawala yamphongo.+ Lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mokondwa.+ Pakuti m’chipululu mudzatumphuka madzi ndipo m’dera lachipululu mudzayenda mitsinje. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:6 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 303 Yesaya 1, ptsa. 374-376, 378-381 Nsanja ya Olonda,2/15/1996, ptsa. 11-12, 16, 18 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 130-132
6 Pa nthawiyo, munthu wolumala adzakwera phiri ngati mmene imachitira mbawala yamphongo.+ Lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mokondwa.+ Pakuti m’chipululu mudzatumphuka madzi ndipo m’dera lachipululu mudzayenda mitsinje.
35:6 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 303 Yesaya 1, ptsa. 374-376, 378-381 Nsanja ya Olonda,2/15/1996, ptsa. 11-12, 16, 18 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 130-132