2 Mbiri 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yotamu+ anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Mayi ake dzina lawo linali Yerusa mwana wa Zadoki.+ 2 Mbiri 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anamanga geti lakumtunda la nyumba ya Yehova+ ndipo pakhoma la mpanda wa Ofeli anamangapo zinthu zambiri.+ Nehemiya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atumiki apakachisi*+ omwe ankakhala ku Ofeli+ anakonza mpandawo mpaka patsogolo pa Geti la Kumadzi,+ kumʼmawa. Iwo anakonzanso nsanja yomwe inatulukira kunja kwa mpanda.
27 Yotamu+ anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Mayi ake dzina lawo linali Yerusa mwana wa Zadoki.+
3 Iye anamanga geti lakumtunda la nyumba ya Yehova+ ndipo pakhoma la mpanda wa Ofeli anamangapo zinthu zambiri.+
26 Atumiki apakachisi*+ omwe ankakhala ku Ofeli+ anakonza mpandawo mpaka patsogolo pa Geti la Kumadzi,+ kumʼmawa. Iwo anakonzanso nsanja yomwe inatulukira kunja kwa mpanda.