-
Zefaniya 3:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Tsiku limenelo Yerusalemu adzauzidwa kuti:
“Usaope iwe Ziyoni,+
Ndipo manja ako asafooke.
17 Yehova Mulungu wako ali pakati panu+
Ndipo adzakupulumutsa chifukwa ndi wamphamvu.
Iye adzakondwera nawe.+
Adzakhala phee chifukwa chokhutira ndi chikondi chimene akukusonyeza,
Ndipo adzafuula mosangalala chifukwa chokondwera nawe.
-