Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Kodi ndi ndani amene wakhulupirira zinthu zimene anamva kwa ife?*+

      Ndipo kodi dzanja la Yehova+ laonetsedwa kwa ndani?+

  • Yohane 12:37, 38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ngakhale kuti anachita zizindikiro zambiri pamaso pawo, iwo sankamukhulupirira, 38 moti mawu a mneneri Yesaya anakwaniritsidwa. Iye anati: “Yehova,* kodi ndi ndani amene wakhulupirira zinthu zimene anamva kwa ife?*+ Ndipo kodi dzanja la Yehova* laonetsedwa kwa ndani?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena