Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma Sihoni sanalole kuti Aisiraeli adutse mʼdziko lake. Mʼmalomwake, iye anasonkhanitsa anthu ake onse nʼkupita kukamenyana ndi Aisiraeli mʼchipululumo. Anakafika ku Yahazi ndipo anayamba kumenyana ndi Aisiraeli.+

  • Yesaya 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Hesiboni ndi Eleyale+ akulira mofuula.

      Mawu awo akumveka mpaka ku Yahazi.+

      Nʼchifukwa chake amuna onyamula zida a ku Mowabu akungofuula.

      Iwo akunjenjemera kwambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena