Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 24:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Atangomaliza ntchitoyo anabweretsa ndalama zimene zinatsala kwa mfumu ndi Yehoyada. Ndalamazo anazigwiritsa ntchito popanga ziwiya zamʼnyumba ya Yehova, ziwiya zogwiritsa ntchito pa utumiki ndi popereka zopereka komanso popanga makapu ndi ziwiya zagolide ndi zasiliva.+ Ndipo ankapereka nsembe zopsereza+ nthawi zonse panyumba ya Yehova masiku onse a Yehoyada.

  • 2 Mbiri 36:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mfumuyo inatenga ziwiya zonse, zazikulu ndi zazingʼono, zamʼnyumba ya Mulungu woona. Inatenganso chuma cha mʼnyumba ya Yehova, chuma cha mfumu ndi cha akalonga ake. Inatenga chilichonse nʼkupita nacho ku Babulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena