Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 79:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Anthu oyandikana nafe akutinyoza,+

      Anthu otizungulira akutiseka komanso kutikuwiza.

  • Yeremiya 48:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 ‘Muledzeretseni+ chifukwa wadzikuza pamaso pa Yehova.+

      Mowabu akugubuduka mʼmasanzi ake,

      Ndipo wakhala chinthu choyenera kuchinyoza.

  • Ezekieli 25:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Uuze Aamoniwo kuti, ‘Imvani mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inu munanena kuti ‘Eyaa! Zakhala bwino.’ Munanena zimenezi malo anga opatulika atadetsedwa, dziko la Isiraeli litasanduka bwinja komanso nyumba ya Yuda itatengedwa kupita ku ukapolo.

  • Zekariya 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mosatekeseka.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pangʼono,+ koma anthu amenewa anakulitsa kwambiri mavuto a anthu angawo.”’+

  • Zekariya 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Atapatsidwa ulemerero, Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene ankakulandani zinthu zanu,+ chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani, akukhudza mwana wa diso langa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena