Ezara 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinanena kuti: “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi kuti ndikweze nkhope yanga kuyangʼana kwa inu Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu zachuluka kupitirira pamutu pathu ndipo machimo athu aunjikana mpaka kumwamba.+ Nehemiya 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Inu mwachita zinthu molungama pa zonse zimene zatichitikira. Mwachita zinthu mokhulupirika koma ife ndi amene tachita zinthu zoipa.+ Danieli 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tachimwa, tachita zinthu zolakwika komanso zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka nʼkusiya kutsatira malamulo ndi zigamulo zanu. Danieli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, tachita zinthu zochititsa manyazi,* mofanana ndi mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.
6 Kenako ndinanena kuti: “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi kuti ndikweze nkhope yanga kuyangʼana kwa inu Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu zachuluka kupitirira pamutu pathu ndipo machimo athu aunjikana mpaka kumwamba.+
33 Inu mwachita zinthu molungama pa zonse zimene zatichitikira. Mwachita zinthu mokhulupirika koma ife ndi amene tachita zinthu zoipa.+
5 Ife tachimwa, tachita zinthu zolakwika komanso zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka nʼkusiya kutsatira malamulo ndi zigamulo zanu.
8 Inu Yehova, tachita zinthu zochititsa manyazi,* mofanana ndi mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.