Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ine ndidzayenda pakati panu ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga.+

  • Yeremiya 30:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Inu mudzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.”+

  • Yeremiya 31:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 “Pangano limene ndidzapangane ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa masiku amenewo ndi ili: Ndidzaika chilamulo changa mwa iwo+ ndipo ndidzachilemba mumtima mwawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga,” akutero Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena