Maliro 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chilango chimene mwana wamkazi wa anthu anga walandira nʼchachikulu kuposa chimene mzinda wa Sodomu unalandira chifukwa cha machimo ake.+Mzinda umenewu unawonongedwa mʼkanthawi kochepa, ndipo panalibe dzanja limene linauthandiza.+ Danieli 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu mwachitadi zimene munachenjeza kuti mudzachitira ifeyo+ ndi atsogoleri athu amene ankatilamulira.* Mwachita zimenezi potigwetsera tsoka lalikulu. Zimene zachitika mu Yerusalemu sizinayambe zachitikapo padziko lonse lapansi.+
6 Chilango chimene mwana wamkazi wa anthu anga walandira nʼchachikulu kuposa chimene mzinda wa Sodomu unalandira chifukwa cha machimo ake.+Mzinda umenewu unawonongedwa mʼkanthawi kochepa, ndipo panalibe dzanja limene linauthandiza.+
12 Inu mwachitadi zimene munachenjeza kuti mudzachitira ifeyo+ ndi atsogoleri athu amene ankatilamulira.* Mwachita zimenezi potigwetsera tsoka lalikulu. Zimene zachitika mu Yerusalemu sizinayambe zachitikapo padziko lonse lapansi.+