Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 1:27, 28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndinaona chinachake chowala ngati siliva wosakanikirana ndi golide,+ chimene chinkaoneka ngati moto umene ukuyaka kuchokera pa chimene chinkaoneka ngati chiuno chake kupita mʼmwamba. Komanso kuchokera mʼchiuno chake kupita mʼmunsi, ndinaona chinachake chooneka ngati moto.+ Pamalo onse omuzungulira panali powala 28 ngati utawaleza+ umene ukuoneka mumtambo pa tsiku la mvula. Umu ndi mmene kuwala kozungulira pamalopo kunkaonekera. Kunkaoneka ngati ulemerero wa Yehova.+ Nditaona zimenezo, ndinagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yanga pansi. Kenako ndinayamba kumva mawu a winawake akulankhula.

  • Ezekieli 3:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Choncho ndinanyamuka nʼkupita kuchigwako ndipo ndinaona kuti ulemerero wa Yehova uli kumeneko.+ Ulemerero umenewu unali wofanana ndi umene ndinauona pafupi ndi mtsinje wa Kebara+ ndipo ndinagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yanga pansi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena