Numeri 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Utengenso abale ako a fuko la Levi, omwe ndi a mtundu wa bambo ako, kuti azikuthandiza. Azitumikira iweyo+ limodzi ndi ana ako pachihema cha Umboni.+ Numeri 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Azikuthandizani komanso azigwira ntchito zawo zonse zapachihema chokumanako, ndipo munthu wamba* aliyense asamayandikire kwa inu.+
2 Utengenso abale ako a fuko la Levi, omwe ndi a mtundu wa bambo ako, kuti azikuthandiza. Azitumikira iweyo+ limodzi ndi ana ako pachihema cha Umboni.+
4 Azikuthandizani komanso azigwira ntchito zawo zonse zapachihema chokumanako, ndipo munthu wamba* aliyense asamayandikire kwa inu.+