14 Kerubi aliyense anali ndi nkhope 4. Nkhope yoyamba inali ya kerubi. Nkhope yachiwiri inali ya munthu. Nkhope yachitatu inali ya mkango ndipo nkhope ya 4 inali ya chiwombankhanga.+
15 Akerubiwo anali angelo omwe aja amene ndinawaona kumtsinje wa Kebara.+ Akerubiwo akanyamuka kukwera mʼmwamba