Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 24:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kenako chizindikiro cha Mwana wa munthu chidzaonekera kumwamba ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni.+ Iwo adzaona Mwana wa munthu+ akubwera pamitambo ya kumwamba ndi mphamvu ndiponso ulemerero waukulu.+

  • Luka 21:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako adzaona Mwana wa munthu+ akubwera mumtambo ndi mphamvu ndiponso ulemerero waukulu.+

  • Yohane 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndipotu palibe munthu amene anakwera kumwamba+ koma Mwana wa munthu yekha, amene anatsika kuchokera kumwambako.+

  • Machitidwe 7:56
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 56 Ndipo ananena kuti: “Taonani! Ndikuona kumwamba kutatseguka, ndipo Mwana wa munthu+ waima kudzanja lamanja la Mulungu.”+

  • Chivumbulutso 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona mtambo woyera. Pamtambopo panali patakhala winawake wooneka ngati mwana wa munthu,+ atavala chisoti chachifumu chagolide kumutu kwake ndipo mʼdzanja lake munali chikwakwa chakuthwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena