Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 2:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ufumu wa nambala 4 udzakhala wolimba ngati chitsulo.+ Mofanana ndi chitsulo chimene chimaphwanya nʼkupera china chilichonse, ufumuwo udzaphwanya nʼkuwonongeratu maufumu ena onsewa.+

  • Danieli 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndinapitiriza kuona masomphenya usiku umenewo ndipo ndinaona chilombo cha nambala 4. Chilombocho chinali choopsa kwambiri, chochititsa mantha komanso champhamvu kwambiri ndipo chinali ndi mano akuluakulu achitsulo. Chinkadya komanso kuphwanyaphwanya chilichonse chimene chinali nacho pafupi ndipo zotsala chinkazipondaponda ndi mapazi ake.+ Chilombochi chinali chosiyana ndi zilombo zina zonse zimene ndinaona poyamba ndipo chinali ndi nyanga 10.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena