Danieli 2:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Ufumu wachinayi+ udzakhala wolimba ngati chitsulo.+ Popeza kuti chitsulo chimaphwanya ndi kupera china chilichonse, ufumuwo udzaphwanya ndi kuswa maufumu ena onsewa mofanana ndi chitsulo chimene chimaswa zinthu.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:40 Ulosi wa Danieli, ptsa. 55-57 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, ptsa. 5-6
40 “Ufumu wachinayi+ udzakhala wolimba ngati chitsulo.+ Popeza kuti chitsulo chimaphwanya ndi kupera china chilichonse, ufumuwo udzaphwanya ndi kuswa maufumu ena onsewa mofanana ndi chitsulo chimene chimaswa zinthu.+