Danieli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kumwamba kuli Mulungu amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani inu Mfumu Nebukadinezara zimene zidzachitike mʼmasiku otsiriza. Maloto anu komanso masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa:
28 Koma kumwamba kuli Mulungu amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani inu Mfumu Nebukadinezara zimene zidzachitike mʼmasiku otsiriza. Maloto anu komanso masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa: