Genesis 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ana a Semu anali Elamu,+ Ashuri,+ Aripakisadi,+ Ludi ndi Aramu.+ Yesaya 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa tsiku limenelo Yehova adzaperekanso dzanja lake kachiwiri kuti atenge anthu ake otsala kuchokera ku Asuri,+ ku Iguputo,+ ku Patirosi,+ ku Kusi,+ ku Elamu,+ ku Sinara,* ku Hamati ndi mʼzilumba zamʼnyanja.+ Yesaya 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndauzidwa masomphenya ochititsa mantha akuti: Mtundu wachinyengo ukuchita zachinyengo,Ndipo mtundu wowononga ukuwononga. Pita ukachite nkhondo, iwe Elamu! Kazungulire mzindawo, iwe Mediya!+ Ndidzathetsa mavuto onse amene mzindawo unachititsa.+
11 Pa tsiku limenelo Yehova adzaperekanso dzanja lake kachiwiri kuti atenge anthu ake otsala kuchokera ku Asuri,+ ku Iguputo,+ ku Patirosi,+ ku Kusi,+ ku Elamu,+ ku Sinara,* ku Hamati ndi mʼzilumba zamʼnyanja.+
2 Ndauzidwa masomphenya ochititsa mantha akuti: Mtundu wachinyengo ukuchita zachinyengo,Ndipo mtundu wowononga ukuwononga. Pita ukachite nkhondo, iwe Elamu! Kazungulire mzindawo, iwe Mediya!+ Ndidzathetsa mavuto onse amene mzindawo unachititsa.+