Danieli 2:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Shadireki,* Misheki* ndi Abedinego+ kuti akhale oyangʼanira ntchito za boma mʼchigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli ankagwira ntchito kunyumba ya mfumu.
49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Shadireki,* Misheki* ndi Abedinego+ kuti akhale oyangʼanira ntchito za boma mʼchigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli ankagwira ntchito kunyumba ya mfumu.