Hoseya 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziko la Asuri silidzatipulumutsa.+ Ife sitidzakwera pamahatchi.+Ndipo sitidzauzanso ntchito ya manja athu kuti: “Inu Mulungu wathu!”Chifukwa inu ndi amene mumachitira chifundo mwana wamasiye.’+
3 Dziko la Asuri silidzatipulumutsa.+ Ife sitidzakwera pamahatchi.+Ndipo sitidzauzanso ntchito ya manja athu kuti: “Inu Mulungu wathu!”Chifukwa inu ndi amene mumachitira chifundo mwana wamasiye.’+