Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 6:26, 27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ine ndikulamula kuti mʼzigawo zonse za ufumu wanga, anthu azinjenjemera chifukwa cha mantha pamaso pa Mulungu wa Danieli.+ Chifukwa iye ndi Mulungu wamoyo ndipo adzakhalapo mpaka kalekale. Ufumu wake sudzawonongedwa komanso ulamuliro wake udzakhalapo kwamuyaya.+ 27 Iye amapulumutsa+ ndi kulanditsa anthu ake, ndipo amachita zizindikiro komanso zinthu zodabwitsa kumwamba ndi padziko lapansi,+ moti wapulumutsa Danieli kwa mikango.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena