Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 60:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chifukwa mtundu uliwonse ndi ufumu uliwonse umene sudzakutumikira udzawonongedwa,

      Ndipo mitundu ya anthu idzasakazidwa kotheratu.+

  • Danieli 2:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Mʼmasiku a mafumu amenewo, Mulungu wakumwamba adzakhazikitsa ufumu+ umene sudzawonongedwa.+ Ufumu umenewu sudzaperekedwa kwa anthu a mtundu wina uliwonse.+ Koma udzaphwanya nʼkuthetsa maufumu ena onsewa+ ndipo ndi ufumu wokhawu umene udzakhalepo mpaka kalekale.+

  • Zefaniya 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova wanena kuti: ‘Choncho pitirizani kundiyembekezera,*+

      Mpaka tsiku limene ndidzanyamuke kuti ndikatenge zinthu za anthu omwe ndawagonjetsa.*

      Chiweruzo changa ndi choti ndisonkhanitse mitundu ya anthu, ndisonkhanitse maufumu,

      Kuti ndiwasonyeze mkwiyo wanga, ndithu mkwiyo wanga wonse woyaka moto,+

      Chifukwa moto wa mkwiyo wanga udzawotcheratu dziko lonse lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena