Yesaya 60:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ana a anthu amene ankakupondereza adzabwera nʼkudzagwada pamaso pako.Anthu onse amene ankakuchitira zachipongwe adzagwada pamapazi ako,Ndipo adzakutchula kuti mzinda wa Yehova,Ziyoni wa Woyera wa Isiraeli.+
14 Ana a anthu amene ankakupondereza adzabwera nʼkudzagwada pamaso pako.Anthu onse amene ankakuchitira zachipongwe adzagwada pamapazi ako,Ndipo adzakutchula kuti mzinda wa Yehova,Ziyoni wa Woyera wa Isiraeli.+